Mnyamata wa zaka 17 Tinasha Mtawali, wadzipha ku Chitipi m’boma la Lilongwe, pa nkhani zomwe zikuganizilidwa kuti ndi za chibwenzi. Mneneri wa polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu wati mnyamatayu adaimbira lamya chibwenzi chake kuchiuza kuti sadzamuonanso. A Chigalu ati ali mkati molankhulana, bwenzi lakelo linamva kuombedwa kwa mfuti ndipo Tinasha adaleka kulankhura. Izi zidapangitsa […]
The post Mnyamata wa zaka 17 azipha poziwombera ndi mfuti kamba kosemphana ndi chibwezi chake appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.