Usi ayankhulapo pa imfa ya Lucius Banda: “Ntchito za Lucius zinali zozama kotero kuti zipitilira kutumikira’

Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Michael Usi wati ndiwokhudzidwa ndi imfa ya mkhalakale mu maimbidwe Soldier Lucius Banda. Mukalata yomwe alemba, a Usi ati akulira limodzi ndi mtsogoleri wadziko lino a Lazarus Chakwera komanso Amalawi onse. Iwo atinso banja la chipani cha UTM lataya munthu yemwe amatsogolera ntchito zokopa anthu mu chipanichi komanso […]

The post Usi ayankhulapo pa imfa ya Lucius Banda: “Ntchito za Lucius zinali zozama kotero kuti zipitilira kutumikira’ appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください