Wapampando wa komiti yoona za malamulo Ku nyumba ya malamulo, Peter Dimba wati komitiyi yapeza kuti mlandu wokhudza Paramount Holdings Limited womwe wozenga milandu wa boma Masauko Chamkakala anawuthesa, upitilire. Dimba wati komitiyi siinakhutitsidwe ndi chigamulo chomwe chinaperekedwa,pa mlandu womwe akulu akulu aku Paramount Holdings Limited inapereka zikalata zabodza Ku sukulu ya ukachenjede yomwe imagula […]
The post Komiti yoona za malamulo ku Parliament yayi mulandu wa Paramount Holdings upitilire appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.