Aphunzitsi omwe adamaliza maphunziro awo kuchokera m’sukulu zosula aphunzitsi akupulayimale zosiyanasiyanasiyana m’dziko muno m’gawo la IPTE 14, 15 ndi 17, koma sadalembedwebe ntchito ndi boma, apempha boma kuti lisamatsogoze ndale koma kukwanilitsa zomwe lidalonjeza. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe aphunzitsiwa alembera maunduna aboma ndipo mwambo opereka kalatazi wachitika dzulo pa 17 May, 2024 kulikulu […]
The post Aphunzitsi alangiza boma kuti lichite zomwe lidalonjeza appeared first on Malawi 24.