Bwalo la milandu ku Lilongwe laimitsa mulandu wa a Shepherd Bushiri komanso mayi akunyumba kwawo a Mary Bushiri omwe akuyankha milandu yomwe adapalamula mdziko la South Africa. Banja la a Busshiri likuyankha milandu yokhudza kuzembetsa ndalama ku South Africa ndipo boma la dzikolo likufuna awiriwa atumizidwe mdzikolo kuti akayankhe milanduyi. Lero mmawa bwalo la milanduli […]
The post Mulandu wa a Bushiri waimitsidwa appeared first on Malawi 24.