Mulandu wa Bushiri awuimitsa mpaka pa July 17 akuti chifukwa otsogolera boma, a Malunda, adwala

Bwalo la Lilongwe chief resident magistrate laimitsa mpaka pa 17 July 2024 kumva mulandu omwe dziko la South Africa likufuna kuti mneneri Shepherd Bushiri ndi mkazi wawo apite mdzikolo kuti akayankhe milandu. Kuimitsaku kwachitika kambakoti yemwe akutsogolera ma loya a mbali yaboma, a Dzikondianthu Malunda wadwala. Lero, oimira a Bushiri amayenera kupitiliza kufunsa mafunso mboni […]

The post Mulandu wa Bushiri awuimitsa mpaka pa July 17 akuti chifukwa otsogolera boma, a Malunda, adwala appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください