Amalawi ayamba kukolola zipatso za ulendo wa mtsogoleri wa dziko lino, Dr. Lazarus McCarthy Chakwera, ku dziko la Belgium mchaka cha 2022 pamene makampani a ku dziko la Belgium tsopano ayamba kugwira ntchito zawo mdziko muno. Imodzi mwa makampani omwe Chakwera adakakumana nawo ku Belgium ndi Phillip Morris yomwe Lachinayi yatsimikizira Amalawi za kudzipereka kwake […]
The post Amalawi ayamba kukolola zipatso za ulendo wa Chakwera ku Belgium appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.