Zangolunjikana ndi sabata yomwe boma laganiza kuchotsa milandu yokhudza za Katangale ya wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko la Malawi a Saulos Chilima ngakhale bungwe lothana ndi Katangale la Anti- Corruption Bureau (ACB) linati lili ndi ma umboni okwanila a zakatangale zomwe a Chilima adachita. A chilima amayimbidwa mulandu woti adalandira chiphuphu kwa wakatangale ochita malonda Zuneth […]
The post A Chakwera akulowela nawo achinyamata ku thengo – watelo kafukufuku appeared first on Malawi 24.