Omenyera ufulu Bon Kalindo, wayamba kuchotsera milandu yomwe akuzengedwa pomwe khothi ku Zomba lalamura kuti nkuluyu ndi mfulu pa mlandu oyambitsa zipolowe omwe amazengedwa m’bomalo. A Kalindo omweso amatchuka ndi dzina lawo la pazisudzo la Winiko, anamangidwa m’bomali pa 23 November chaka chatha pomwe zionetsero zomwe anatsogolera m”boma la Zomba zinathera zipolowe. M’mwezi wa January […]
The post Kalindo ampeza osalakwa appeared first on Malawi 24.