Mtsogoleri wa bungwe la National Women’s Football a Adelaide Migogo wati mphoto imodzi yomwe Malawi yapeza yomwe wawina Leticia Chinyamula kukhala osewela yemwe adzakhale wapamwamba mtsogolomu zawonetsa kuti osewerawa ali ndi kuthekera kochita bwino kwambiri mtsogolomu akamalowa nawo mu mipikisano yambiri. Poyankhula ndi wayilesi ina m’dziko muno a Migogo apempha boma kuti lithandize mpira wa […]
The post Mpira wa miyendo wa atsikana ukuyenda bwino – Migogo appeared first on Malawi 24.