Bungwe lowona za zisankho la Malaŵi Electoral Commission (MEC) lanenetsa kuti kuyenda bwino kwa zisankho zapatatu mu 2025 kudalira kuti anthu amvetse bwino ndondomeko ya kayendetsedwe kazisankhozi. M’modzi mwa makomishonala a bungweli, Dr Anthony Mukumbwa, anena izi lachinayi ku Mzimba pa msonkhano wolimbikitsa mafumu, atsogoleri a mipingo, mabungwe a Civil Society (CSOs) ndi ena onse […]
The post Ndife wokonzeka kuchititsa zisankho – MEC appeared first on Malawi 24.