Mgwirizano ndi DPP ndiotheka- Mtambo

Mtsogoleri wa gulu la Citizens For Transformation (CFT), a Timothy Mtambo ati ndiokonzeka kugwilira ntchito limodzi ndi Democratic Progressive Party (DPP), chipani chimene anatengapo gawo kuti chichoke mu ulamuliro wa dziko la Malawi mu chaka cha 2019.  A Mtambo amayankhula izi pa wayilesi ya Zodiak mu pologalamu ya padera yomwe yaulutsidwa Lachiwiri pa 7 May, […]

The post Mgwirizano ndi DPP ndiotheka- Mtambo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください