Apampando mzigawo zinayi za chipani cha MCP alembera mlembi wamkulu mchipanichi a Elsenhower Mkaka kuwawuza kuti sakugwirizana ndi zomwe anena kuti ofesi yawo idzayamba yaunika kaye anthu olowa mchipanichi asadavomerezedwe. Anayiwa ndi a Zebron Chilondola, a Joseph Chavula, a Peter Simbi komanso a Augustine Chidzanja. Akuluakuluwa ati akutsutsana ndi ganizo lomwe linapangidwalo ndipo ati ngati […]
The post Kwavuta ku MCP pomwe akuluakulu ena mchipanichi adzudzula a Mkaka paganizo lakayendesedwe ka Convention appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.