Khama lipindura: Mneneri Habakkuk yemwe, pafupipafupi, wakhala akupempha Shepherd Bushiri kuti amuthandize ndi K1 miliyoni yokha, waona ngati kutulo pomwe wapatsidwa K6 miliyoni ndi mneneri nzakeyu. Habakkuk yemwe dzina lake lenileni ndi Stanford Sinyangwe, sadzayiwala tsiku La mulungu pa 5 May, 2024 kamba koti mneneri Bushiri anamuchitira chinthu chomwe wakhala akumupempha. Patsikuli, Bushiri amachititsa mapemphero […]
The post Zitsulo kunolana: Bushiri athandiza mneneri Habakkuk kupeza K1 miliyoni appeared first on Malawi 24.