A Polisi ya Jenda m’boma la Mzimba, amanga anthu awiri omwe ndi Julius Zgambo (27) ndi Alfred Zimba (22) kamba kolima chamba popanda Chilolezo ku Vibangalala m’bomalo. M’neneri wa Polisi ya Jenda, Sub Inspector Macfarlen Mseteka, wauza Malawi24 kuti awiriwa anamangidwa usiku wa pa 5–6 May 2024, a Polisi atasinidwa khutu kuti amalima chamba m’derali. […]
The post Awiri amangidwa chifukwa cholima chamba ku Mzimba appeared first on Malawi 24.