Bungwe la boma lobweleketsa ngongole la (NEEF) lapempha a khristu kuti adzibweza ngongole zomwe amatenga ku bungweli komanso mabungwe ena opereka ngongole. Mmodzi mwa akuluakulu owona nkhanizi a Humphrey Thondolo, ndiye wanena izi Lamulungu madzulo pa mpingo wa Area 25 Assemblies of God pa maphunziro okhudza mene ndondomeko ya ngongole imayendera. Malinga ndi a […]
The post Bungwe lobwerekesa ndalama la NEEF lapempha Akhristu mdziko muno kuti azibwedza ngongole appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.