Banki ya FDH yakweza ndalama za mpikisano wa FDH Bank Cup kuchoka pa K120 million kufika pa K150 million. Mkulu owona za malonda ku bankiyi, a Ronald Chimchere wanena izi kumwambo opereka mphoto kwa osewera komanso atolankhani amene adachita bwino mu mpikisanowu chaka chatha. Pakadalipano, mwambowu uli mkati ku hotela ya Amaryllis mzinda wa Blantyre. […]
The post Koma kumeneko!FDH Cup panopa yafika pa K150million kuchoka pa K120m appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.