Ophunzira pa Mzuni alanga wakuba

M’nyamata wina amene wakhala akunamizira kuti ndi ophunzira pasukulu ya Ukachenjede ya Mzuzu ali mu uluru osaneneka kutsatira kumenyedwa ndi ophunzira pasukukuyi pomuganizira kuti anaba mafoni awiri awophunzira ena. Amon Chimalawalana, yemwe watiuza nkhaniyi, wati lero pasukuluyi panali masewero ndipo ophunzira omwe anali kusewera mpira anasunga mafoni awo pa malo ena ndipo atatuluka anapeza kuti […]

The post Ophunzira pa Mzuni alanga wakuba appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください