Mtsutso wabuka pa masamba a nchezo pa nkhani ya chizindikiro cha chipani chomwe changobadwa kumene cha People’s Development Party (PDP). Chipanichi, chomwe mtsogoleri wake ndi membala wakale wa chipani cha Democratic Progressive Party (DPP), Kondwani Nankhumwa, chagwiritsa ntchito mbalame ya Nkhwazi ngati chizindikiro chake. Pomwe anthu ena sakuonapo vuto, ena akuti ma kampani ena amagwiritsa […]
The post Chizindikiro cha chipani chatsopano chiutsa mtsutso appeared first on Malawi 24.