Mtsongoleri wazipani zotsutsa boma kunyumba yamalamulo yemwenso ndi phungu wanyumba yamalamulo wa dera lapakati m’boma la Mulanje Kondwani Nankhumwa walengeza kuti wayambitsa chipani chake cha People’s Development Party (PDP). A Nankhumwa, womwe anachotsedwa mu chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) alengeza izi patsamba lawo la mchenzo la Facebook. Nankhumwa wanena kuti apangitsa msonkhano wa atolankhani […]
The post Ku Malawi kwabadwa chipani china Cha PDP appeared first on Malawi 24.