La fote limakwanabe, Bambo ku Kasungu anjatidwa atabvulidwa chigoba

Bambo wa zaka 23, ali m’chitokosi cha apolisi m’boma la Kasungu pomwe akuyembekezeleka kuyankha mlandu ofuna kuba mu dzina la polisi. Bamboyu yemwe dzina lake ndi Lonjezo Banda, wagwidwa usiku wa lachinayi akufuna kulanda njinga za moto kwa oyendetsa kabaza ponamizila kuti iyeyo ndi polisi ofisala. Pamodzi ndi nzawo wina, ma lipoti akuti bambo Banda […]

The post La fote limakwanabe, Bambo ku Kasungu anjatidwa atabvulidwa chigoba appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください