Chipani cha Alliance for Democracy (Aford) chati chili ndi chikhulupiliro kuti chidzapambana chikadzaima pa chokha pa chisankho cha mtsogoleri wa dziko cha chaka cha mawa. Wofalitsa nkhani za chipanichi a Amatullah Annie Maluwa auza Nyasatimes kuti kwa zaka zitatu tsopano chipanichi chakula mphamvu zimene zikupereka chirimbikitso kuti chidzaime pa chokha. A Maluwa ati kutuluka kwa […]
The post Aford yasindika kuti izayima payokha ndipo yanenetsa kuti izatenga upulezidenti wa dziko lino appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.