Bushiri wagawa chimanga ku mawanja okhudzidwa ndi madzi osefukira ku Mangochi

Pomwe miyanda miyanda ya anthu omwe amakhala mphepete mwa nyanja ya dziko lino akhudzidwa ndi vuto lakusefukira kwa madzi, mtsogoleri wampingo wa Enlightened Christian Gathering, mneneri Shepherd Bushiri wagawa chimanga ku mawanja okhudzidwa oposa 200 ku Mangochi. Anthu ambiri omwe amakhala mphepete mwa nyanja ya Malawi, asamukira kaye m’madera akumtunda kamba kakusefukira kwa nyanjayi zomwe […]

The post Bushiri wagawa chimanga ku mawanja okhudzidwa ndi madzi osefukira ku Mangochi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください