Alimi a fodya adandaula ati sakulandirabe ndalama zawo ngakhale anagulisa fodya kalekale

Alimi a fodya omwe anagulitsa fodya wao sabata loyamba la msika wafodya adandaula kuti sanalandirebe ndalama zawo pomwe msika walowa sabata yachiwiri. Mmodzi mwa alimiwa a Msaiwale Zakaliya omwe analinso ndi anzawo ena oposa khumi aku Chamama m’boma la Kasungu ati ali kakasi chifukwa adatumiza msanga fodya kuti atumize ana ku sukulu. Iwo ati malamulo […]

The post Alimi a fodya adandaula ati sakulandirabe ndalama zawo ngakhale anagulisa fodya kalekale appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください