Yadya 1 pa YouTube ndi Controller

Mtengo wautali salozerana ndipo nyimbo yomwe yadya nambala one pa YouTube ndi ija ya mkulu odikula uku akutudzula mbina maka ikafika paja akumati “She got me feeling like ah ah ah ah ah ah!”  Tsopano nyimboyi yaoneredwa ka 1.4 miliyoni msabata ziwiri zokha zomwe ndizopatsa chidwi. Sabata ziwiri zokha ndi zomwe zadutsa chitulutsileni kanema wa […]

The post Yadya 1 pa YouTube ndi Controller appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください