Boma la Dr Lazarus Chakwera awunikanso maphunziro ndi cholinga choti afanane ndi zolinga za Malawi agenda 2063

Boma la Dr Lazarus McCarthy Chakwera likusintha dongosolo la zamaphunziro ndi cholinga chakuti maphunziro adzifanana ndi dongosolo la ndondomeko ya boma ya Agenda 2063. Izi zikutanthauza kuti m’malo moti ophunzira azikhala otanganidwa kuloweza ziwalo za ziwala iwo azitanganidwa ndi kuphunzira maluso osiyana siyana monga kakonzedwe ka magalimoto, kusoka zovala , kukhoma zidebe ndi maluso ena […]

The post Boma la Dr Lazarus Chakwera awunikanso maphunziro ndi cholinga choti afanane ndi zolinga za Malawi agenda 2063 appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください