Zachitikanso ku Dedza: Bambo amenya mkazi wake mpaka kufa

Patangodusa mwezi umodzi pomwe bamboo wina anawombera mkazi mpaka imfa ku Dedza, thambo lakuda lagwanso mubomali pomwe mayi wina m’mudzi mwa Yahaya pa boma ku Dedza wafa atamenyedwa ndi mamuna wake. Mfumu Yahaya yauza Nyasatimes kuti mayiyu ndi mamuna wake onse anali ku mowa dzulo koma anayamba kukangana kumeneko kamba koti mkazi wake amalankhula ndi […]

The post Zachitikanso ku Dedza: Bambo amenya mkazi wake mpaka kufa appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください