Nkhondo yosumilana yavuta: naye Mneneri Chisa Mbele wapanikizana ndi Kampanikiza

Komatu kulibe kupuma ku ma bwalo. Ili mkamwakamwa ya Dorothy Shonga osumira Mayi Easter Gondwe, a Joshua Chisa Mbele nawo awopseza kuti akamang’ala ku bwalo kuti a Gerald Kampanikiza akuwayipitsira mbiri. Malingana ndi zimene alemba pa tsamba lawo a Chisa Mbele, ati ngati sachotsa mauthenga owazembelera kuti iwo ndi kathyali. Mu sabatayi, kunamveka kuti bambo […]

The post Nkhondo yosumilana yavuta: naye Mneneri Chisa Mbele wapanikizana ndi Kampanikiza appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください