Nduna yakale ya za masewero mu ulamuliro wachipani cha United Democratic Front (UDF) a Moses Dossi yamwalira. Mwana wamalemuwa Susan wati a Dossi amwalira kuchipatala cha Blantyre Adventist kucha kwa Lachinayi ali ndi zaka 70 ndipo wati adzawakumbikira bambo wake chifukwa adali munthu okonda mtendere komanso okonda aliyense. A Dossi, omwenso adakhalapo phungu wakunyumba yamalamulo […]
The post Nduna yakale ya za masewero mu ulamuliro wachipani cha UDF yamwalira appeared first on Malawi 24.