Mtsogoleri wakale wa dziko lino, Joyce Banda, walangiza mzika za dziko lino kusamala chimanga kamba ka njala yoopsa yomwe iyale mphasa chaka chino chifukwa cha kusintha kwa nyengo. A Banda ayankhula izi Lachitatu ku Domasi komwe amapereka chakudya, zikwama komaso kukhazikitsa ntchito yokonzanso zinthu zina ndi zina pa Gala pulayimale sukulu ndipo ati pakufunika machawi […]
The post Samalani chakudya, kuli njala- Joyce Banda appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 