Mnyamata wina yemwe amayankha mlandu kale, wamangidwaso kachiwiri pamodzi ndi mzake wina yemwe amafuna kukamupatsira chamba chomwe anachibisa munkhwayira tsiku lakumva mlandu. Malingana ndi ofalitsa nkhani pa Polisi ya Zomba, a Patricia Supuliano, oganizilidwa awiriwa ndi Estery Evance wa zaka 19 komaso Bonface Phiri wa zaka 22. A Supuliano ati izi zachitika Lachiwiri pa 16 […]
The post Awiri anjata pofuna kulowetsa chamba ku ndende appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 