President wa dziko lino, a Lazarus Chakwera, ati alimi akuyenera kulondoloza fodya wawo moyenera cholinga choti ena asalemere powabera alimiwa potengera kuti ulimi wa fodya umafunika chidwi komanso kulondoloza chilichonse mu nthawi yoyenera. A Chakwera anena izi pa msonkhano omwe anapangitsa pa sukulu ya pulayimale ya Vivya kwa mfumu yaikulu Njombwa ku Kasungu pomwe amatsegurira […]
The post Alimi muyenera kulondoloza fodya wanu kuti ena asalemelere ndi umbava otibera -atero a Chakwera appeared first on Malawi 24.