A Chinoko Banda, yemwe ndi m’modzi mwa alimi omwe amalima komanso kugulitsa fodya, wadandaura kuti kukwera kwa zipangizo za ulimi wa fodya monga feteleza kamba kakugwa kwa kwacha, kwapangitsa kuti alimi adzipeza phindu lochepa pa nthawi yogulitsa Fodya. Banda wanena izi pamene President Lazarus Chakwera amatsegurira malonda a fodya ku msika wa Chinkhoma ku Kasungu. […]
The post Kugwa kwacha, kukwera kwa zipangizo za ulimi wa fodya kukupweteka alimi-watero Banda appeared first on Malawi 24.