Chakwera atsekulira misika ya fodya ku Kasungu lero

Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera agwira ntchito zosiyana siyana m’boma la Kasungu lero kuwonjezerapo kutsegulira m’sika wa fodya, malingana ndi chikalata watulutsa mlembi wamkulu wa boma mayi Colleen Zamba. A Chakwera akuyembekezeka kuyendera nyumba za asirikali a nkhondo zomwe boma la Malawi Congress (MCP) lamanga ku Engineering Battalion. Malingana ndi chikalatachi, mtsogoleri wa dziko […]

The post Chakwera atsekulira misika ya fodya ku Kasungu lero appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください