Bungwe la MBS lati lipanga chipikisheni cha machesi osavomerezeka pa msika

Bungwe la Malawi Bureau of Standards (MBS) lati likhala likupanga chipikisheni mu misika komanso mawokala wonse m’dziko muno pofuna kuchotsa pa msika mitundu ya machesi omwe sanavomelezedwe ndi bungweli. M’chikatala chomwe bungweli latulutsa  chati mitundu yina ya machesi monga Paka, Tinga, Kasuku , Mo komanso Soccer yomwe ikupezeka pa misika ya m’dziko muno siyili mukawundula […]

The post Bungwe la MBS lati lipanga chipikisheni cha machesi osavomerezeka pa msika appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください