Boma lalangizidwa kusiya kupeleka ndalama mu ndondomeko ya mtukula pakhomo

Bungwe la a katswiri pa nkhani za zachuma la Financial Market Dealers Association (FIMDA), lalangiza boma la Malawi kuti liganize zosiya kupeleka ndalama mu ndondomeko ya mtukula pa khomo ndi kuyamba kupeleka zinthu ngati chimanga, ufa ndi zina.  Izi ndi malingana ndi mtsogoleri wa bungwe la FIMDA a Leslie Fatch omwe amayankhula Lachisanu munzinda wa […]

The post Boma lalangizidwa kusiya kupeleka ndalama mu ndondomeko ya mtukula pakhomo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください