Mbava yavulazidwa ndi nyesi ikuba mawaya a magetsi

Bambo wina wa zaka 32 ku Blantyre, ali muululu owopsya pa chipatala cha Queen Elizabeth munzinda wa Blantyre pomwe wavulazidwa ndi nyesi za magetsi pomwe akuganizilidwa kuti amafuna kuba mawaya a magetsi. Malingana ndiwofalitsa nkhani pa polisi ya Limbe, Sergeant Aubrey Singanyama, bambo oganizilidwa kubayu wazindikilidwa ngati a Dickson Khoviwa omwe akuti akumana ndi zakudazi […]

The post Mbava yavulazidwa ndi nyesi ikuba mawaya a magetsi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください