Itaphulika nkhani yokhudza mchitidwe wa aphunzitsi a sukulu ya ukachenjede ya Mzuzu University kugonana ndi ophunzira pofuna kusinthana ndi malikisi kuti akhonze, sukuluyi tsopano yayamba kufufuza kuti apeze yemwedi akuchiti izi. Sukuluyi yatsindika izi mu chikalata chake kuti ikulondola mwa chidwi nkhani imene yafala mu masamba a mchezo yokhudza aphunzitsi ena pa sukuluyi omwe amauza ophunzira […]
The post Kafukufuku watentha ku Mzuzu University pa nkhani ya Malikisi ndi chisembwere appeared first on Malawi 24.