Amangidwa kamba ka kupha mzake mchaka cha 2015

Mawu oti mulandu si uwola aphelezera pomwe Apolisi ku Bolero m’boma la Rumphi amanga Giuele Mfune pomuganizira kuti adapha Magowa Mtambo mchaka cha 2015. A Mfune akhala akuthawa kuyambira 2015 ndipo amangidwa anthu akufuna kwabwino atatsina khutu apolisi zakupezeka kwa a Mfune ku Bolero . Malinga ndi m’neneri wa polisi ku Rumphi Sub Inspector Noel […]

The post Amangidwa kamba ka kupha mzake mchaka cha 2015 appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください