Chiwerengero cha anthu omwalira ndi ‘ambuye mtengeni’ chafika pa 8

Ofesi ya zaumoyo munzinda wa Blantyre yati chiwerengero cha anthu omwe afa m’dera la Manase kamba komwa mowa osadziwika bwino omwe ukutchedwa ‘ambuye mtengeni’ kapena kuti ‘magagada’, chafika pa asanu ndi atatu (8). Izi ndi malingana ndi ofalitsa nkhani ku ofesi ya zaumoyo mu nzindawu a Chrissy Banda omwe ati kukwera kwa chiwerengeroku kukutsatira kumwalira […]

The post Chiwerengero cha anthu omwalira ndi ‘ambuye mtengeni’ chafika pa 8 appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください