Apolisi mu mzinda wa Blantyre amanga yemwe anali mtolankhani wakale wa Malawi24 McMillan Mhone, kamba kolemba nkhani yokhudza munthu woganiziridwa katangale a Abdul Karim Batatawala chaka chatha. Pa 15 August chaka chatha, Malawi24 idatulutsa nkhani yomwe imakamba zambiri zokhudza momwe a Batatawala akuganizilidwira kuti anaphwanya malamulo kuti apeze ma kontalakiti ndi boma la Malawi. M’nkhaniyo, […]
The post Mtolankhani wakale wa Matawi24 wamangidwa polemba nkhani yokhudza oganizilidwa katangale Batatawala appeared first on Malawi 24.