Kwachema kwa Manase ku Blantyre pamene apolisi ayamba kunjata anthu onse omwe akugulitsa mowa omwe ndi owopsa ndipo ukutchulidwa ndi mayina monga: Ambuye tengeni, magaga, komanso taya njinga omwe pakadali pano waphapo anthu asanu (5). Malingana ndi mneneri wa apolisi m’chigawo chakummwera, a Joseph Sauka, ati ntchitoyi ili mkati pamene apolisi afikakale kuderali komwe akulanda […]
The post Apolisi ayamba kunjata anthu ogulitsa mowa wa “Ambuye Tengeni” appeared first on Malawi 24.