Apolisi anjata mayi kamba kotentha ndikuvulaza mwana wake

A polisi m’boma la Dowa akusunga mchitolokosi a Chimwemwe Kayera azaka 35 zakubadwa, kamba kowaganizira kuti anawotcha ndi kuvulaza mwana wawo wamamuna wa zaka khumi ndi ziwiri (12). Mneneri wa Polisi ya Dowa a Seageant Alice Sitima auza Malawi24 kuti nkhaniyi inachitika Lachinayi pa 4 April 2024 nthawi ya 7 kaloko madzulo mmudzi mwa Chiwoza […]

The post Apolisi anjata mayi kamba kotentha ndikuvulaza mwana wake appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください