Apolisi akusaka anthu okwiya omwe agwetsa nyumba, kuba katundu ku Mbayani

A polisi munzinda wa Blantyre ati akusaka anthu ena omwe agwetsa nyumba ndi kuba katundu wa banja lina ku Mbayani poganizira kuti mwana wa m’banjamo wapha mnyamata wina kamba kokana kuchita naye mchitidwe wa mathanyura. Izi ndi malingana ndi wachiwiri kwa ofalitsa nkhani pa polisi ya Blantyre Constable Marry Chiponda omwe atitsimikizira kuti Lachinayi, ku […]

The post Apolisi akusaka anthu okwiya omwe agwetsa nyumba, kuba katundu ku Mbayani appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください