MET yalosera mvula mwezi uno, madzi osefukira ku mpoto

Nthambi yowona za nyengo ndi kusintha kwa nyengo ya Department of Climate Change and Meteorological Services (DCCMS), yati madera ena mdziko muno alandira mvula yopyoola muyeso mwezi uno ndipo pali chiopsezo cha madzi osefukira m’madera ena mchigawo cha ku mpoto. Izi ndi malingana ndi mauthenga a za nyengo omwe nthambiyi yatulutsa Lachiwiri pa 2 April, […]

The post MET yalosera mvula mwezi uno, madzi osefukira ku mpoto appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください