A Polisi amanga mzimayi, abambo awiri kamba kopezeka ndi chamba

A Polisi kwa Jenda m’boma la Mzimba amanga mayi wina ndi amuna awiri chifukwa chopezeka ndi fodya wa Chamba pamalo otchedwa Luviri m’bomali pomwe amadikira galimoto kuti apite ndi katunduyu ku Lilongwe. Malinga ndi ofalitsa nkhani za polisi ya Jenda a Macfarlen Mseteka, atatuwa ndi a Pililani Phiri a zaka 46, a Stanley Mologeni a […]

The post A Polisi amanga mzimayi, abambo awiri kamba kopezeka ndi chamba appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください