Bambo wina yemwe dzina lake ndi Mathews Zichepe Banda wa zaka 37 ali mmanja mwa apolisi ku Lingadzi, pomuganizira kuti wakhala akubera anthu a kabaza njinga za kapalasa powamwetsa mankhwala ophera tizilombo otchedwa boric acid ku Lilongwe. Malingana ndi Mneneri wa polisi ya Lingadzi, Cassim Manda, pa 25 March cha m’ma 9 koloko m’mawa, mkuluyu […]
The post Bambo amangidwa kaamba kobera akabaza appeared first on Malawi 24.