Anyamata ofuna kupita ku Israel akwiyira boma Kamba kowachedwesa kupita

Achinyamata okwiya asonkhana pa manda a Kamuzu ku Lilongwe pomwe akufuna kuyamba ulendo wawo opita ku nyumba ya chifumu {Kamuzu Palace} kuti akatule madandaulo awo pa nkhani ya ulendo wawo waku Israel. Iwo akuti adapanga zonse zoyenera monga kupangitsa ma passport kuti akagwire ntchito ku minda yaku Israel koma ndondomekoyi ikuchedwa ndipo akuona kuti zalowa […]

The post Anyamata ofuna kupita ku Israel akwiyira boma Kamba kowachedwesa kupita appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください