Prophet Shepherd Bushiri yemwe ndi mtsogoleri wa mpingo wa ECG – The Jesus Nation, lero wagawa chimanga kwa anthu opitilira 1300 mdera la Sub-T/A Nkhanga m’boma la Nkhotakota. Polankhula pa mwambo ogawa chimangacho kudzera kwa mneneri wawo, a Aubrey Kusakala, prophet Bushiri wati ndiokhudzidwa kwambiri ndi kutaika kwa miyoyo komaso kuonongeka kwa katundu kamba ka […]
The post Bushiri wagawa Chimanga ku Nkhotakota appeared first on Malawi 24.