Anthu ochita malonda ochokera kwa Chinseu m’dera la Zomba Lisanjala anachita m’bindikiro ku office ya Escom mu mzinda wa Zomba powonetsa mkwiyo wao kuti akhala miyezi isanu opanda magetsi potsatira kupsa kwa transformer mdelaro. Poyankhula ndi Malawi24, m’modzi mwa anthu omwe akutsogolera pochita m’bindikirowo a Leonard Phiri ati cholinga chawo akufuna kuti bungwe la Escom […]
The post Anthu a ku Chingale achita m’bindikiro ku ofesi ya Zomba Escom appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 